imbani fonimwaulere 54747 - unicef 19 poster in... · covid 19 posters 2020 chichewa.cdr author:...
TRANSCRIPT
Tsekani pakamwa ndi mphuno potsokomola kapena kuyetsemula ndi kansalu, kapena popinda mkono wanu ndi kutsokomolera
kapena kuyetsemulira m'kati mwa mkonowo pamene mwaupindapo.
Matenda a Coronavirus ndiwopeweka
Produced by Health Education Services of the Ministry of Health
Imbani foni
mwaulere
54747
World HealthOrganization
Sambani m’manja ndi Sopo moyenera nthawi zonse
kuti mupewe matenda a Coronavirus.
Matenda a Coronavirus ndiwopeweka
Produced by Health Education Services of the Ministry of Health
Imbani foni
mwaulere
54747
World HealthOrganization
Anyamata ndi asungwana sambani m’manja ndi Sopo nthawi
zonse kuti mupewe matenda a Coronavirus.
Matenda a Coronavirus ndiwopeweka
Produced by Health Education Services of the Ministry of Health
Imbani foni
mwaulere
54747
World HealthOrganization
Makolo titengepo gawo posambitsa ana m’manja ndi sopo nthawi zonse kuti tipewe matenda a Coronavirus
Matenda a Coronavirus ndiwopeweka
Produced by Health Education Services of the Ministry of Health
Imbani foni
mwaulere
54747
World HealthOrganization